Ezekieli 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Udzabweranso ndi Gomeri+ ndi magulu ake onse a asilikali, komanso ndi ana a Togarima+ ochokera kumadera akutali kwambiri a kumpoto. Iwo adzabwera ndi magulu awo onse a asilikali. Chotero iwe udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu.+
6 Udzabweranso ndi Gomeri+ ndi magulu ake onse a asilikali, komanso ndi ana a Togarima+ ochokera kumadera akutali kwambiri a kumpoto. Iwo adzabwera ndi magulu awo onse a asilikali. Chotero iwe udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu.+