-
Ezekieli 38:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iwe udzabwera mʼdzikolo ngati mphepo yamkuntho kudzawaukira. Iweyo, magulu a asilikali ako onse, pamodzi ndi anthu ambiri a mitundu ina, mudzaphimba dzikolo ngati mitambo.”’
-