Ezekieli 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe udzabwera m’dzikolo ngati mphepo yamkuntho.+ Iweyo, magulu ako onse a asilikali, pamodzi ndi anthu ambiri a mitundu ina, mudzaphimba dzikolo ngati mitambo.”’+
9 Iwe udzabwera m’dzikolo ngati mphepo yamkuntho.+ Iweyo, magulu ako onse a asilikali, pamodzi ndi anthu ambiri a mitundu ina, mudzaphimba dzikolo ngati mitambo.”’+