Ezekieli 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthuyo anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, uonetsetse, umvetsere mwatcheru ndipo uchite chidwi ndi zonse* zimene ndikuonetse, chifukwa ndakubweretsa kuno kuti udzachite zimenezi. Ukauze nyumba ya Isiraeli zonse zimene uone.”+
4 Munthuyo anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, uonetsetse, umvetsere mwatcheru ndipo uchite chidwi ndi zonse* zimene ndikuonetse, chifukwa ndakubweretsa kuno kuti udzachite zimenezi. Ukauze nyumba ya Isiraeli zonse zimene uone.”+