-
Ezekieli 40:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako anayeza khonde la kanyumba kapageti nʼkupeza kuti linali mikono 8. Anayezanso zipilala zake zamʼmbali, nʼkupeza kuti zinali mikono iwiri. Khonde la kanyumbako linali kumbali imene inayangʼanizana ndi kachisi.
-