-
Ezekieli 40:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anayeza khonde la kanyumba ka pachipata n’kupeza kuti linali mikono 8. Zipilala zake zam’mbali zinali mikono iwiri. Khonde la kanyumbako linali loyang’ana kubwalo lakunja.
-