Ezekieli 40:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 7+ ndipo khonde lake linali kutsogolo kwa masitepewo. Kumbali iliyonse ya khondelo kunali chipilala chimodzi ndipo pazipilalazo panali zithunzi za mtengo wa kanjedza.
26 Munthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 7+ ndipo khonde lake linali kutsogolo kwa masitepewo. Kumbali iliyonse ya khondelo kunali chipilala chimodzi ndipo pazipilalazo panali zithunzi za mtengo wa kanjedza.