Ezekieli 40:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kanyumba kameneka kanali ndi masitepe 7 okwerera m’chipatacho,+ ndipo kutsogolo kwawo kunali khonde. Pazipilala zimene zinali m’mbali mwa khondelo, chimodzi mbali iyi ndi china mbali inayo, panali zithunzi za mtengo wa kanjedza.
26 Kanyumba kameneka kanali ndi masitepe 7 okwerera m’chipatacho,+ ndipo kutsogolo kwawo kunali khonde. Pazipilala zimene zinali m’mbali mwa khondelo, chimodzi mbali iyi ndi china mbali inayo, panali zithunzi za mtengo wa kanjedza.