-
Ezekieli 40:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Kenako anandipititsa mʼbwalo lamkati kudzera pageti lakumʼmwera. Atayeza kanyumba kapageti kakumʼmwera anapeza kuti miyezo yake inali yofanana ndi tinyumba tina tija.
-