-
Ezekieli 40:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Kenako ananditengera m’bwalo lamkati kudzera pachipata cha kum’mwera. Munthu uja anayeza kanyumba ka pachipata cha kum’mwera ndipo miyezo yake inali yofanana ndi tinyumba tina tija.
-