29 Miyezo ya zipinda za alonda za kanyumba kapagetiko, zipilala zake zamʼmbali ndi khonde lake inali yofanana ndi ya tinyumba tina tija. Kumbali iliyonse ya kanyumbako komanso khonde lake kunali mawindo. Kanyumbako kanali mikono 50 mulitali ndi mikono 25 mulifupi.+