-
Ezekieli 40:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Miyezo ya zipinda za alonda za kanyumba ka pachipatako, zipilala zake zam’mbali ndi khonde lake inali yofanana ndi miyezo ya tinyumba tina tija. Kanyumba ka pachipata konseko ndi khonde lake zinali ndi mawindo. M’litali mwake kanyumba kameneka kanali mikono 50 ndipo m’lifupi mwake kanali mikono 25.+
-