-
Ezekieli 40:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Matebulo 4 a nsembe zopsereza zathunthuwo anali amiyala yosema. Mulitali mwake anali mkono umodzi ndi hafu, mulifupi mwake anali mkono umodzi ndi hafu ndipo kuchoka pansi kufika pamwamba anali mkono umodzi. Pamatebulo amenewa ankaikapo zida zophera nyama ya nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.
-