-
Ezekieli 40:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Matebulo anayi a nsembe zopsereza zathunthuwo anali amiyala yosema. M’litali mwake anali mkono umodzi ndi hafu, m’lifupi mwake anali mkono umodzi ndi hafu ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba anali aatali mkono umodzi. Pamatebulo amenewa analinso kuikapo zida zophera nyama ya nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.
-