Ezekieli 40:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kunja kwa kanyumba kapageti kamkati kunali zipinda zodyeramo oimba.+ Zipindazi zinali mʼbwalo lamkati pafupi ndi geti lakumpoto ndipo zinayangʼana kumʼmwera. Chipinda china chinali pafupi ndi geti lakumʼmawa ndipo chinayangʼana kumpoto.
44 Kunja kwa kanyumba kapageti kamkati kunali zipinda zodyeramo oimba.+ Zipindazi zinali mʼbwalo lamkati pafupi ndi geti lakumpoto ndipo zinayangʼana kumʼmwera. Chipinda china chinali pafupi ndi geti lakumʼmawa ndipo chinayangʼana kumpoto.