Ezekieli 41:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anayeza khoma la kachisi ndipo anapeza kuti kuchindikala kwake linali mikono 6. Zipinda zamʼmbali kuzungulira kachisi yenseyo zinali mikono 4 mulifupi.+
5 Kenako anayeza khoma la kachisi ndipo anapeza kuti kuchindikala kwake linali mikono 6. Zipinda zamʼmbali kuzungulira kachisi yenseyo zinali mikono 4 mulifupi.+