Ezekieli 41:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anayezanso kuchindikala kwa khoma la nyumbayo ndipo anapeza kuti linali mikono 6. M’lifupi mwa chipinda cham’mbali munali mikono inayi. Umu ndi mmene zinalili kuzungulira nyumba yonseyo.+
5 Anayezanso kuchindikala kwa khoma la nyumbayo ndipo anapeza kuti linali mikono 6. M’lifupi mwa chipinda cham’mbali munali mikono inayi. Umu ndi mmene zinalili kuzungulira nyumba yonseyo.+