-
Ezekieli 41:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndinaona kuti kachisi yenseyo anamumanga pamaziko okwera. Maziko a zipinda zamʼmbali anali bango lathunthu, yomwe ndi mikono 6, kuchokera pansi kukafika polumikizira.
-