Ezekieli 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinaona kuti nyumba yonseyo anaimanga pamaziko aatali omwe anachita khonde kuzungulira nyumbayo. Kutalika kwa maziko a zipinda zam’mbali kunali bango lathunthu, lalitali mikono 6 kuchokera pansi kukafika polumikizira.+
8 Ndinaona kuti nyumba yonseyo anaimanga pamaziko aatali omwe anachita khonde kuzungulira nyumbayo. Kutalika kwa maziko a zipinda zam’mbali kunali bango lathunthu, lalitali mikono 6 kuchokera pansi kukafika polumikizira.+