Ezekieli 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu uja anayeza kachisi nʼkupeza kuti anali mikono 100 mulitali. Ndipo malo opanda kanthu aja, nyumba ija* ndi makoma ake zinalinso mikono 100 mulitali.
13 Munthu uja anayeza kachisi nʼkupeza kuti anali mikono 100 mulitali. Ndipo malo opanda kanthu aja, nyumba ija* ndi makoma ake zinalinso mikono 100 mulitali.