-
Ezekieli 41:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Munthu uja anayeza kachisi n’kupeza kuti anali mikono 100 m’litali mwake. Anayezanso mpata waukulu umene unali mbali zonse za kachisiyo, nyumba imene inali kumadzulo kwake ndi makoma ake, ndipo zonse pamodzi zinali mikono 100 m’litali.
-