Ezekieli 41:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 malo apafupi ndi khomo, mawindo a mafelemu aakulu mkati koma aangʼono kunja+ ndiponso timakonde timene tinali mʼmalo atatuwo. Pafupi ndi malo apakhomowo anakhomapo matabwa+ kuchokera pansi kufika mʼmawindo, ndipo mawindowo anali otchinga.
16 malo apafupi ndi khomo, mawindo a mafelemu aakulu mkati koma aangʼono kunja+ ndiponso timakonde timene tinali mʼmalo atatuwo. Pafupi ndi malo apakhomowo anakhomapo matabwa+ kuchokera pansi kufika mʼmawindo, ndipo mawindowo anali otchinga.