Danieli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikukutamandani komanso kukuyamikani, inu Mulungu wa makolo anga,Chifukwa mwandipatsa nzeru ndi mphamvu. Ndipo tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani,Mwatidziwitsa zinthu zimene mfumu ikuda nazo nkhawa.”+
23 Ndikukutamandani komanso kukuyamikani, inu Mulungu wa makolo anga,Chifukwa mwandipatsa nzeru ndi mphamvu. Ndipo tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani,Mwatidziwitsa zinthu zimene mfumu ikuda nazo nkhawa.”+