Danieli 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Utangoyamba kupemphera Mulungu anandiuza uthenga, ndiye ndabwera kudzakufotokozera uthengawo chifukwa ndiwe munthu wokondedwa kwambiri.*+ Choncho mvetsera mwatcheru zimene ndikufuna kukuuza ndipo umvetse masomphenyawa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 7, 184-186
23 Utangoyamba kupemphera Mulungu anandiuza uthenga, ndiye ndabwera kudzakufotokozera uthengawo chifukwa ndiwe munthu wokondedwa kwambiri.*+ Choncho mvetsera mwatcheru zimene ndikufuna kukuuza ndipo umvetse masomphenyawa.