Hoseya 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinalankhula ndi aneneri,+Ndipo ndinawaonetsa masomphenya ambiri.Ndinalankhula mafanizo kudzera mwa aneneri.
10 Ndinalankhula ndi aneneri,+Ndipo ndinawaonetsa masomphenya ambiri.Ndinalankhula mafanizo kudzera mwa aneneri.