Yoweli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inu ana aamuna a Ziyoni sangalalani chifukwa cha Yehova Mulungu wanu.+Iye adzakupatsani mvula yoyambirira pa mlingo woyenera,Ndipo adzakugwetserani mvula yamvumbi,Mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza, ngati mmene zinalili poyamba.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:23 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 17-18
23 Inu ana aamuna a Ziyoni sangalalani chifukwa cha Yehova Mulungu wanu.+Iye adzakupatsani mvula yoyambirira pa mlingo woyenera,Ndipo adzakugwetserani mvula yamvumbi,Mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza, ngati mmene zinalili poyamba.+