-
Mika 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mbadwa zotsala za Yakobo zidzakhala pakati pa mitundu yambiri ya anthu.
Zidzakhala pakati pa anthu ambiri.
Ngati mkango pakati pa nyama zakutchire.
Komanso ngati mkango wamphamvu pakati pa magulu ankhosa,
Umene umadutsa pakati pa nkhosazo nʼkuzimbwandira ndiponso kuzikhadzula
Ndipo palibe wozipulumutsa.
-