Nahumu 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zishango za amuna amphamvu zaviikidwa mu utoto wofiira,Asilikali ake avala zovala zofiira kwambiri. Zitsulo za magaleta ake ankhondo zili waliwali ngati moto,Pa tsiku limene akukonzekera nkhondo.Ndipo mikondo ya mitengo ya junipa* aipukuta.
3 Zishango za amuna amphamvu zaviikidwa mu utoto wofiira,Asilikali ake avala zovala zofiira kwambiri. Zitsulo za magaleta ake ankhondo zili waliwali ngati moto,Pa tsiku limene akukonzekera nkhondo.Ndipo mikondo ya mitengo ya junipa* aipukuta.