-
Nahumu 2:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mfumu idzaitanitsa asilikali ake amaudindo akuluakulu.
Iwo azidzapunthwa pamene akuthamanga,
Adzathamangira kumpanda wa mzinda.
Iwo adzakhwimitsa chitetezo.
-