Nahumu 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumu idzakumbukira asilikali ake amphamvu.+ Iwo adzathamangira kumpanda wa mzinda ndipo pamene akutero adzakhala akupunthwa.+ Pamenepo mpanda wachitetezo udzakhala ndi chitetezo champhamvu.
5 Mfumu idzakumbukira asilikali ake amphamvu.+ Iwo adzathamangira kumpanda wa mzinda ndipo pamene akutero adzakhala akupunthwa.+ Pamenepo mpanda wachitetezo udzakhala ndi chitetezo champhamvu.