-
Nahumu 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nkhani imeneyi ndi yotsimikizirika. Mzindawo wavulidwa nʼkuchititsidwa manyazi,
Anthu ake atengedwa ndipo akapolo ake aakazi akulira.
Akumveka ngati nkhunda pamene akudziguguda pamtima.
-