Nahumu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhani imeneyi yatsimikiziridwa. Mzindawo udzavulidwa ndi kuchititsidwa manyazi, ndipo anthu ake adzatengedwa.+ Akapolo ake aakazi adzakhala akulira ngati nkhunda+ ndipo adzadziguguda pachifuwa.+
7 Nkhani imeneyi yatsimikiziridwa. Mzindawo udzavulidwa ndi kuchititsidwa manyazi, ndipo anthu ake adzatengedwa.+ Akapolo ake aakazi adzakhala akulira ngati nkhunda+ ndipo adzadziguguda pachifuwa.+