Habakuku 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye popeza vinyo ndi wachinyengo,Munthu wodzikuza sadzakwaniritsa cholinga chake. Iye amangolakalakabe ngati Manda,*Ndipo samakhutira ngati imfa. Iye amabweretsa mitundu yonse ya anthu,Ndipo amawasonkhanitsa kuti akhale ake.+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 102/1/2000, tsa. 155/15/1989, ptsa. 24-25
5 Ndiye popeza vinyo ndi wachinyengo,Munthu wodzikuza sadzakwaniritsa cholinga chake. Iye amangolakalakabe ngati Manda,*Ndipo samakhutira ngati imfa. Iye amabweretsa mitundu yonse ya anthu,Ndipo amawasonkhanitsa kuti akhale ake.+