Habakuku 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wakonza zoti uchititse manyazi nyumba yako. Ndipo ukudzilakwira popha anthu a mitundu yambiri.+