Zefaniya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aneneri ake ndi amwano ndiponso achinyengo.+ Ansembe ake amaipitsa zinthu zopatulika,+Ndipo amaphwanya malamulo.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 21-225/1/1991, ptsa. 19-20
4 Aneneri ake ndi amwano ndiponso achinyengo.+ Ansembe ake amaipitsa zinthu zopatulika,+Ndipo amaphwanya malamulo.+