Zefaniya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzasonkhanitsa anthu amene akumva chisoni chifukwa chosapezeka pazikondwerero zako.+Iwo sanali ndi iwe chifukwa anali ku ukapolo kumene ankanyozedwa.+
18 Ndidzasonkhanitsa anthu amene akumva chisoni chifukwa chosapezeka pazikondwerero zako.+Iwo sanali ndi iwe chifukwa anali ku ukapolo kumene ankanyozedwa.+