Zefaniya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Anthu ogwidwa ndi chisoni+ amene sanapezeke pa zikondwerero zako ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Iwo sanali ndi iwe chifukwa anali kudziko lachilendo kumene anali kutonzedwa.+
18 “Anthu ogwidwa ndi chisoni+ amene sanapezeke pa zikondwerero zako ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Iwo sanali ndi iwe chifukwa anali kudziko lachilendo kumene anali kutonzedwa.+