Salimo 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Misozi yanga yasanduka chakudya changa usana ndi usiku,+Pamene anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima. Maliro 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wapasula chisimba*+ chake ngati chisimba cha m’munda+ ndipo wathetsa zikondwerero zake.Yehova wachititsa kuti zikondwerero+ ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo mu mkwiyo wake waukulu wakana mfumu ndi wansembe.+
3 Misozi yanga yasanduka chakudya changa usana ndi usiku,+Pamene anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.
6 Iye wapasula chisimba*+ chake ngati chisimba cha m’munda+ ndipo wathetsa zikondwerero zake.Yehova wachititsa kuti zikondwerero+ ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo mu mkwiyo wake waukulu wakana mfumu ndi wansembe.+