Yobu 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+ Yeremiya 52:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+ Aroma 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Mulungu alibe tsankho.+
19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+
24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+