Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima. Hoseya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo ndidzathetsa kusangalala kwake konse.+ Ndidzathetsa zikondwerero zake,+ chikondwerero cha tsiku lokhala mwezi,+ cha sabata ndi chikondwerero china chilichonse. Zefaniya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Anthu ogwidwa ndi chisoni+ amene sanapezeke pa zikondwerero zako ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Iwo sanali ndi iwe chifukwa anali kudziko lachilendo kumene anali kutonzedwa.+
4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.
11 Pamenepo ndidzathetsa kusangalala kwake konse.+ Ndidzathetsa zikondwerero zake,+ chikondwerero cha tsiku lokhala mwezi,+ cha sabata ndi chikondwerero china chilichonse.
18 “Anthu ogwidwa ndi chisoni+ amene sanapezeke pa zikondwerero zako ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Iwo sanali ndi iwe chifukwa anali kudziko lachilendo kumene anali kutonzedwa.+