Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+

  • Salimo 78:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+

      Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+

  • Yesaya 63:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kwa kanthawi kochepa, anthu anu oyera+ anali ndi zinthu. Koma adani athu apondaponda malo anu opatulika.+

  • Yesaya 64:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nyumba yathu yoyera ndiponso yokongola+ imene makolo athu anali kukutamandiranimo,+ yasanduka chinthu chofunika kuchitentha pamoto,+ ndipo zinthu zathu zonse zabwinozabwino+ zasakazidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena