Salimo 80:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 N’chifukwa chiyani mwagwetsa mpanda wake wamiyala?+Ndipo n’chifukwa chiyani anthu onse odutsa mumsewu akuthyola zipatso zake?+ Salimo 89:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mwagwetsa makola ake onse amiyala.+Mizinda yake yamipanda yolimba mwaisandutsa mabwinja.+ Yesaya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wamkazi wa Ziyoni+ wasiyidwa ngati msasa m’munda wa mpesa, ngati chisimba* m’munda wa minkhaka, ndiponso ngati mzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+
12 N’chifukwa chiyani mwagwetsa mpanda wake wamiyala?+Ndipo n’chifukwa chiyani anthu onse odutsa mumsewu akuthyola zipatso zake?+
8 Mwana wamkazi wa Ziyoni+ wasiyidwa ngati msasa m’munda wa mpesa, ngati chisimba* m’munda wa minkhaka, ndiponso ngati mzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+