Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho Hezekiya mfumu ya Yuda anatumiza uthenga kwa mfumu ya Asuri ku Lakisi, wakuti: “Ndachimwa. Siyani kundiukira. Ndikupatsani chilichonse chimene mungandilamule.”+ Chotero mfumu ya Asuri inalamula Hezekiya mfumu ya Yuda kuti apereke matalente* 300 a siliva+ ndi matalente 30 a golide.

  • Yesaya 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye analima mundawo n’kuchotsamo miyala, kenako anabzalamo mphesa zofiira zabwino kwambiri. Anamanga nsanja pakati pa mundawo.+ Anasemamonso choponderamo mphesa.+ Iye anali kuyembekezera kuti mundawo ubereka mphesa zabwino,+ koma unabereka mphesa zam’tchire.+

  • Yesaya 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ndipo idzadutsa mu Yuda yense. Idzadutsa ngati madzi osefukira,+ ndipo idzafika mpaka m’khosi.+ Idzatambasula mapiko ake+ mpaka m’lifupi mwa dziko lako, iwe Emanueli.”+

  • Yeremiya 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwo akhala ngati alonda a kunja kwa mzinda ndipo azungulira Yerusalemu kumbali zonse+ kuti amuukire chifukwa chakuti wandipandukira,”+ watero Yehova.

  • Luka 19:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda+ wazisonga+ kukuzungulira.+ Adaniwo adzakutsekereza ndi kukusautsa+ kuchokera kumbali zonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena