-
Zekariya 5:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno anandiuza kuti: “Ili ndi temberero limene likubwera padziko lonse lapansi, chifukwa aliyense amene akuba,+ mogwirizana ndi zimene zalembedwa kumbali imodzi ya mpukutuwo, sakulandira chilango. Komanso aliyense amene akulumbira mwachinyengo,+ mogwirizana ndi zimene zalembedwa kumbali ina ya mpukutuwo, sakulandira chilango.
-