Zekariya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndinafunsa kuti: “Nʼchiyani chimenechi?” Iye anandiyankha kuti: “Chimenechi ndi chiwiya chokwana muyezo wa efa.”* Ndiyeno anapitiriza kuti: “Anthu oipa amaoneka chonchi padziko lonse lapansi.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 24
6 Choncho ndinafunsa kuti: “Nʼchiyani chimenechi?” Iye anandiyankha kuti: “Chimenechi ndi chiwiya chokwana muyezo wa efa.”* Ndiyeno anapitiriza kuti: “Anthu oipa amaoneka chonchi padziko lonse lapansi.”