Zekariya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndinafunsa kuti: “N’chiyani chimenechi?” Iye anandiyankha kuti: “Chimenechi ndi chiwiya choyezera chokwana muyezo wa efa.”* Ndiyeno anapitiriza kunena kuti: “Umu ndi mmene amaonekera anthu oipa a padziko lonse lapansi.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 24
6 Choncho ndinafunsa kuti: “N’chiyani chimenechi?” Iye anandiyankha kuti: “Chimenechi ndi chiwiya choyezera chokwana muyezo wa efa.”* Ndiyeno anapitiriza kunena kuti: “Umu ndi mmene amaonekera anthu oipa a padziko lonse lapansi.”