Zekariya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno nditayangʼana kumwamba ndinaona azimayi awiri akubwera. Azimayiwo ankauluka mphepo ikuwomba ndipo mapiko awo anali ooneka ngati a dokowe. Iwo ananyamula chiwiya chija nʼkupita nacho mʼmwamba.* Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, ptsa. 24-25
9 Ndiyeno nditayangʼana kumwamba ndinaona azimayi awiri akubwera. Azimayiwo ankauluka mphepo ikuwomba ndipo mapiko awo anali ooneka ngati a dokowe. Iwo ananyamula chiwiya chija nʼkupita nacho mʼmwamba.*