-
Zekariya 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ngakhale kuti pa nthawiyo anthu omwe adzatsale adzaona kuti zimenezo nʼzosatheka, kodi zidzakhalanso zosatheka kwa ine?’ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”
-