Zekariya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ngakhale kuti m’masiku amenewo otsalira a anthu awa adzaona kuti zimenezo n’zosatheka, kodi zidzakhalanso zosatheka kwa ine?’+ watero Yehova wa makamu.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:6 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 16-17
6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ngakhale kuti m’masiku amenewo otsalira a anthu awa adzaona kuti zimenezo n’zosatheka, kodi zidzakhalanso zosatheka kwa ine?’+ watero Yehova wa makamu.”