Yobu 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndadziwa kuti inu mumatha kuchita zinthu zonse,+Ndipo palibe zimene simungakwanitse.+ Yeremiya 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ine ndine Yehova, Mulungu wa anthu onse.+ Kodi kwa ine pali nkhani ina iliyonse yovuta?+ Maliko 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu anawayang’ana ndi kuwauza kuti: “Kwa anthu n’zosathekadi, koma sizili choncho kwa Mulungu, pakuti zinthu zonse n’zotheka ndi Mulungu.”+ Luka 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anawauza kuti: “Zinthu zosatheka ndi anthu n’zotheka ndi Mulungu.”+
27 Yesu anawayang’ana ndi kuwauza kuti: “Kwa anthu n’zosathekadi, koma sizili choncho kwa Mulungu, pakuti zinthu zonse n’zotheka ndi Mulungu.”+